Edited Chichewa languages
This commit is contained in:
parent
acca2f4055
commit
785b9086dd
279
locales/ny.yaml
279
locales/ny.yaml
@ -1,103 +1,103 @@
|
||||
welcomeHeading: "Takulandirani ku Machankura"
|
||||
productAmountPrompt: "Kodi mugula ndalama zingati za {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} kwa {{{recipient}}}"
|
||||
productAmountPrompt: "Kodi mugula {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} ochuluka bwanji kwa {{{recipient}}}"
|
||||
amountRangeText: "(osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})"
|
||||
inCurrencyPrompt: "(mu {{{currencyTicker}}})"
|
||||
inputAmountOutOfRangePrompt: "Simungathe kugula ma airtime kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa"
|
||||
inputAmountOutOfRangePrompt: "Simungathe kugula ma yunitsi kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa"
|
||||
inputAmountOutOfRangeProductPrompt: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa"
|
||||
pleaseTryAgain: "Chonde yesaninso."
|
||||
pleaseTryAgain: "Chonde yeseraninso."
|
||||
menu: "Menyu"
|
||||
inputAmountImpossible: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} ndi zolemba zomwe zilipo {{{amountInput}}}"
|
||||
inputAmountImpossible: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} ndi zolembedwazi {{{amountInput}}}"
|
||||
enterMachankuraPinForAirtime: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{inputAmountValue}}} {{{productCurrencyTicker}}} ({{{btcAmount}}} {{{currencyTicker}}}) {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} kwa {{{phoneNumber}}}"
|
||||
failedToConfirmAction: "Sikunakwanitse kutsimikizira zomwe mwachita. Chonde yesaninso."
|
||||
inputAmountInvalid: "Ndalama sizikugwirizana. Chonde yesaninso."
|
||||
productPurchaseInitiated: "Mwayambitsa kugula {{{categoryType}}}. Onani mbiri ya malonda kuti mumve zambiri."
|
||||
productPurchaseFailed: "Kugula {{{categoryType}}} kunalephera. Chonde yesaninso."
|
||||
yourPhoneNumberNotSupported: "Nambala yanu ya foni {{{airtimeReceipent}}} panopa ilibe zinthu zomwe tingathandize kubereka."
|
||||
pinDontMatch: "PIN yanu ya Machankura siyikugwirizana ndi PIN yomwe ili mu dongosolo lathu. Chonde yesaninso."
|
||||
balanceTooLow: "Mulingo wanu wa ndalama ndi wochepa kwambiri kuti muchite izi. Chonde yesaninso."
|
||||
purchaseFailed: "Sikunatheke kugula. Chonde yesaninso."
|
||||
phoneNumberNotSupported: "Nambala ya foni siyikugwirizana. Chonde yesaninso."
|
||||
failedToConfirmAction: "Simunakwanitse kutsimikizira zomwe mwachita. Chonde yeseraninso."
|
||||
inputAmountInvalid: "Ndalama sizikugwirizana. Chonde yeseraninso."
|
||||
productPurchaseInitiated: "Kugula kwayambika." {{{categoryType}}}. Onani ma transaction kuti mudziwe zambiri."
|
||||
productPurchaseFailed: "Kugula {{{categoryType}}} kwalephereka. Chonde yeseraninso."
|
||||
yourPhoneNumberNotSupported: "Nambala yanu ya foni {{{airtimeReceipent}}} panopa ilibe zinthu zomwe tingathandize kupereka."
|
||||
pinDontMatch: "PIN yanu ya Machankura siyikugwirizana ndi PIN yomwe ili mu dongosolo lathu. Chonde yeseraninso."
|
||||
balanceTooLow: "Ndalama zanu zotsala ndi zochepa kwambiri kuti muchite izi. Chonde yeseraninso."
|
||||
purchaseFailed: "Sizinatheke kugula. Chonde yeseraninso."
|
||||
phoneNumberNotSupported: "Nambala ya foni siyikugwirizana. Chonde yeseraninso."
|
||||
pickYourNetwork: "Sankhani netiweki yanu"
|
||||
pickNetworkFailure: "Sitinatheke kugwira ntchito yosankha netiweki. Chonde yesaninso."
|
||||
pickNetworkFailure: "Sizinatheke kusankha netiweki. Chonde yeseraninso."
|
||||
phoneNumber: "Nambala ya Foni"
|
||||
lightningAddress: "Adilesi ya Lightning"
|
||||
lightningAddressPrompt: "(Kwa wolemba pang'onopang'ono, ingolemba dzina la ogwiritsa ntchito ndipo patsamba lotsatira lowetsani domain)"
|
||||
lightningAddressPrompt: "(Kwa wolemba pang'onopang'ono, ingolembani dzina la ogwiritsa ntchito ndipo patsamba lotsatira lowetsani domain)"
|
||||
machankuraUsername: "Dzina la ogwiritsa ntchito"
|
||||
unsupported: "sizikuthandizidwa"
|
||||
mostRecent: "Zaposachedwa Kwambiri"
|
||||
mostFrequent: "Zomwe Zimachitika Kawirikawiri"
|
||||
unsupported: "pakanalibe"
|
||||
mostRecent: "Zongochitika posachedwa"
|
||||
mostFrequent: "Zochitika kawirikawiri"
|
||||
inputReceipentToBuy: "Chonde lowetsani {{{recipientText}}} yemwe mukufuna kugula {{{bitrefillProductName}}} kwa:"
|
||||
vendorNotFound: "Sitinapeze wogulitsa malinga ndi zomwe mwalemba. Chonde yesaninso."
|
||||
vendorNotFound: "Sitinapeze wogulitsa malinga ndi zomwe mwalemba. Chonde yeseraninso."
|
||||
enterPinToSend: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mutumize {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}:"
|
||||
lowBalancePleaseIncrease: "Mulingo wanu wa ndalama ({{{balance}}} {{{currencyTicker}}}) ndi wochepa kwambiri. Onjezerani ndalama kapena mutumize zochulukirapo kuposa {{{amountText}}}"
|
||||
cannotSendToYourself: "Simungathe kutumiza ndalama kwa inu nokha. Chonde yesaninso ndi wolandila wina."
|
||||
successfullySent: "Mwatumiza bwino {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}."
|
||||
failedToSend: "Sikunatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso."
|
||||
successfullyGiftedSats: "Mwathandizira {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Ali ndi masiku 21 kuti apeze mphatso yanu, chonde muwauze kuti ayambe akaunti ya Machankura."
|
||||
failedToGiftSats: "Sikunatheke kuthandiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso ndi mitengo ina."
|
||||
giftCountryUnsupported: "Simungathebe kugawa Bitcoins kwa nambala za foni m'mayiko amenewo."
|
||||
failedTransfer: "Sikunatheke kusamutsa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso."
|
||||
initiatedTransfer: "Kutumiza kwanu kwa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} kwayamba. Onani ma transaction anu kuti mudziwe zambiri."
|
||||
failedTransferLightningAddress: "Sikunatheke kusamutsa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso kapena adilesi ina ya lightning."
|
||||
lowBalanceForServiceFeePleaseIncrease: "Mulingo wanu wa ndalama ({{{satsBalance}}} sats) ndi wochepa kwambiri kuti mupereke chindapusa cha ntchito ({{{feeText}}}). Onjezerani ndalama kapena mutumize zocheperako kuposa {{{amountText}}}"
|
||||
aztecoVoucherAlreadyRedeemed: "Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) idakali yobwezeretsedwa."
|
||||
redeemAztecoVoucherPrompt: "Tikukonzekera kubweza Azteco voucher wamtengo wa {{{satsAmount}}} sats ku akaunti yanu ya Machankura."
|
||||
redeem: "Bwezerani"
|
||||
decline: "Kukana"
|
||||
failedToRedeemAztecoVoucher: "Sikunatheke kubweza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso."
|
||||
failedToProcessAztecoVoucher: "Sikunatheke kukonza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso."
|
||||
failedToAccessAztecoVoucher: "Sikunatheke kupeza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso."
|
||||
initiatedAztecoOnchainRedemption: "Mwayambitsa kubwezera. Azteco onchain voucher akubweza."
|
||||
errorGeneratingOnchainAddress: "Cholakwika chamkati pakupanga adilesi. Chonde yesaninso."
|
||||
redemptionInProgress: "Kubwezera kukuyenda. Chonde dikirani."
|
||||
reattemptAztecoRedemptionTitle: "Mwayesanso kubwezera"
|
||||
reattemptAztecoRedemptionBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) akubwezera Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
|
||||
redeem1ForYouTitle: "Mwayambitsa kubwezera"
|
||||
redeem1ForYouBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) akubwezera Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
|
||||
successfullyInitiatedRedemption: "Mwayambitsa bwino kubwezera kwa Azteco voucher (mudzalandira {{{amountInSatoshis}}} sats). Mudzalandira zatsopano zokhudzana ndi kusamutsa."
|
||||
failedToFindAztecoVoucher: "Sikunatheke kupeza Azteco voucher {{{aztecoVoucherCode}}}"
|
||||
declinedRedemption: "Mwakana kubweza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}})."
|
||||
lowBalancePleaseIncrease: "Ndalama zanu zotsala ({{{balance}}} {{{currencyTicker}}}) ndi zochepa kwambiri. Onjezerani ndalama zotsala kapena mutumize zocheperapo zosapitilira {{{amountText}}}"
|
||||
cannotSendToYourself: "Simungathe kudzitumizira ndalama nokha. Chonde yeseraninso kutumizira wina."
|
||||
successfullySent: "Mwakwanitsa kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}."
|
||||
failedToSend: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso."
|
||||
successfullyGiftedSats: "Mwakwanitsa kugawa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Ali ndi masiku 21 kuti alandire mphatso yanu. Chonde auzeni kuti atsegule akaunti ya Machankura poimba mwaulere *384*8333*0265#."
|
||||
failedToGiftSats: "Sizinatheke kugawa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso ndi mlingo wina."
|
||||
giftCountryUnsupported: "Simungathe kugawa ma Bitcoin kwa manambala za foni m'dziko limenelo."
|
||||
failedTransfer: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso."
|
||||
initiatedTransfer: "Kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} kwayambika. Onani ma transaction anu kuti mudziwe zambiri."
|
||||
failedTransferLightningAddress: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso kapena tumizani ku adilesi ina ya lightning."
|
||||
lowBalanceForServiceFeePleaseIncrease: "Ndalama zanu ({{{satsBalance}}} sats) ndi zochepa kwambiri ({{{feeText}}}). Chonde onjezerani ndalama kapena tumizani zocheperako, zosapitilira {{{amountText}}}"
|
||||
aztecoVoucherAlreadyRedeemed: "Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) yawomboledwa kale."
|
||||
redeemAztecoVoucherPrompt: "Tikukonzekera kuwombola Azteco voucher yamtengo wa {{{satsAmount}}} sats ku akaunti yanu ya Machankura."
|
||||
redeem: "Wombolani"
|
||||
decline: "Letsani"
|
||||
failedToRedeemAztecoVoucher: "Sizinatheke kuwombola Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
|
||||
failedToProcessAztecoVoucher: "Sizinatheke kukonza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
|
||||
failedToAccessAztecoVoucher: "Sizinatheke kupeza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
|
||||
initiatedAztecoOnchainRedemption: "Mwayamba kuwombola. Azteco onchain voucher ikuwomboledwa."
|
||||
errorGeneratingOnchainAddress: "Kupanga address kwakanika. Chonde yeseraninso."
|
||||
redemptionInProgress: "Ntchito yowombola ilim'kati. Chonde dikirani."
|
||||
reattemptAztecoRedemptionTitle: "Mukuyeseranso kuwombola"
|
||||
reattemptAztecoRedemptionBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) ikuwombola Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
|
||||
redeem1ForYouTitle: "Mwayamba kuwombola"
|
||||
redeem1ForYouBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) ikuwombola Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
|
||||
successfullyInitiatedRedemption: "Mwakwanitsa kayamba kuwombola Azteco voucher (mudzalandira {{{amountInSatoshis}}} sats). Mulandira zotsatira."
|
||||
failedToFindAztecoVoucher: "Sizinatheke kupeza Azteco voucher {{{aztecoVoucherCode}}}"
|
||||
declinedRedemption: "Mwakana kuwombola Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}})."
|
||||
sendBTC: "Tumizani BTC"
|
||||
receiveBTC: "Landirani BTC"
|
||||
balanceAndHistory: "Mulingo ndi zambiri"
|
||||
barterBTC: "Barter Goods/Services"
|
||||
settings: "Zokonda"
|
||||
balanceAndHistory: "Ndalama zotsala komanso zambiri"
|
||||
barterBTC: "Kugula katundu/kulipira"
|
||||
settings: "Zothandizira"
|
||||
exit: "Tulukani"
|
||||
username: "Dzina la ogwiritsa ntchito"
|
||||
pin: "PIN"
|
||||
language: "Chilankhulo"
|
||||
pin: "PIN/ nambala ya chinsinsi"
|
||||
language: "Chiyankhulo"
|
||||
learnMore: "Phunzirani zambiri"
|
||||
enterPinToUpdateUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti musinthe dzina lanu la ogwiritsa ntchito la adilesi ya lightning"
|
||||
enterPinToSetUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mukhazikitse dzina la ogwiritsa ntchito la adilesi yanu ya lightning:"
|
||||
enterUsername: "Lowetsani malemba omwe mukufuna monga dzina lanu latsopano la ogwiritsa ntchito:"
|
||||
usernameUpdated: "Dzina lanu la ogwiritsa ntchito lasinthidwa kukhala {{{proposedUsernameText}}}. Adilesi yanu ya lightning tsopano ndi {{{proposedUsernameText}}}@{{{domain}}}."
|
||||
enterDifferentUsername: "Sikugwirizana kusintha dzina la ogwiritsa ntchito. Chonde lowetsani dzina lina la ogwiritsa ntchito ({{{proposedUsernameText}}} ndi {{{errorStatus}}}):"
|
||||
languageSettingsComingSoon: "Zokonda zilankhulo zikubwera posachedwa."
|
||||
learnMoreSettingsComingSoon: "Zokonda zophunzirira zambiri zikubwera posachedwa."
|
||||
resetPinCountDown: "Mudzatha kukonzanso PIN yanu kuchokera {{{when}}} tsopano. Chonde bwerani patsamba lino pambuyo pake."
|
||||
cancelPinReset: "Kuti mubwezere kubwezeretsa PIN, lowetsani PIN yanu yamakono"
|
||||
enterPinToUpdateUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti musinthe dzina lanu la ogwiritsa ntchito la address ya lightning"
|
||||
enterPinToSetUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti muyike dzina la ogwiritsa ntchito la adilesi yanu ya lightning:"
|
||||
enterUsername: "Sankhani dzina lomwe mukufuna kukhala dzina lanu latsopano la ogwiritsa ntchito:"
|
||||
usernameUpdated: "Dzina lanu la ogwiritsa ntchito lasinthidwa kukhala {{{proposedUsernameText}}}. Address yanu ya lightning tsopano ndi {{{proposedUsernameText}}}@{{{domain}}}."
|
||||
enterDifferentUsername: "Sizinatheke kusintha dzina la ogwiritsa ntchito. Chonde lowetsani dzina lina ({{{proposedUsernameText}}} ndi {{{errorStatus}}}):"
|
||||
languageSettingsComingSoon: "Zosintha chiyankhulo zikubwera posachedwa."
|
||||
learnMoreSettingsComingSoon: "Zokhudza kuphunzirira zambiri, zikubwera posachedwa."
|
||||
resetPinCountDown: "Mudzatha kusintha PIN yanu kuchokera {{{when}}} tsopano. Chonde bwerani patsamba lino pambuyo pake."
|
||||
cancelPinReset: "Kuti muletse kubwezeretsa PIN, lowetsani PIN yanu ya Machankura"
|
||||
cancelledPinReset: "Pempho lanu lobwezeretsa PIN layimitsidwa. Zikomo pogwiritsa ntchito Machankura."
|
||||
pinUpdated: "PIN yanu ya Machankura yasinthidwa kukhala yomwe mwangoyiyika."
|
||||
enterNewPin: "Lowetsani PIN yanu yatsopano yamakilogalamu 5:"
|
||||
expiredPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwatha. Yesaninso."
|
||||
enterNewPin: "Lowetsani PIN yanu yatsopano yazilembo 5:"
|
||||
expiredPinReset: "Nthawi yosinthira PIN yadutsa. Chonde yeseraninso."
|
||||
pinManagement: "Kasamalidwe ka PIN ya Machankura"
|
||||
changePin: "Sinthani PIN"
|
||||
resetPin: "Kubwezeretsa PIN (muiwala PIN)"
|
||||
resetPinPrompt: "Kuti mubwezeretse PIN yanu (chifukwa mwaiwala PIN yanu), muyenera kuyambitsa ndondomeko ya maola 24 (imatha maola 48)."
|
||||
startPasswordReset: "Yambani kubwezeretsa mawu achinsinsi"
|
||||
initiatedPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwakhazikitsidwa. Mudzatha kukhazikitsa mawu achinsinsi atsopano m'maola 24. Kuti muyime pempho, mutha kulowa PIN yanu yamakono."
|
||||
failedPinResetInitiation: "Sikunatheke kuyambitsa kubwezeretsa PIN. Chonde yesaninso."
|
||||
enterCurrentPin: "Lowetsani PIN yanu yamakono:"
|
||||
unitOfMeasurePrompt: "Mukatani (kuyeza kwa mtengo) mungakonde kutumiza sats kwa {{{receiver}}}?"
|
||||
amountToSendPrompt: "Lowetsani kuchuluka kwa {{{selectedCurrencyTicker}}}{{{minimumMaximumRange}}} komwe mukufuna kutumiza kwa {{{receiver}}}:"
|
||||
mediumToSendPrompt: "Kodi mukufuna kutumiza sats kuti:"
|
||||
noPastRecipients: "Palibe omwe alandila pa mndandanda. Chonde lowetsani wolandila kudzera pa nambala ya foni, adilesi ya lightning, kapena dzina la ogwiritsa ntchito."
|
||||
resetPinPrompt: "Kuti mubwezeretse PIN yanu (chifukwa mwaiwala PIN yanu), muyenera kuyamba ndondomeko yosinthira ya maola 24 (imatha maola 48)."
|
||||
startPasswordReset: "Yambani kubwezeretsa nambala yachinsinsi (PIN)"
|
||||
initiatedPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwakhazikitsidwa. Mudzakwanitsa kuyika nambala yachinsinsi yatsopano m'maola 24. Kuti muyimitse pempho lanu, mutha kulowa PIN yanu yamakono."
|
||||
failedPinResetInitiation: "Sizinatheke kuyamba kubwezeretsa PIN. Chonde yeseraninso."
|
||||
enterCurrentPin: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura yomwe mumagwiritsa nthchito:"
|
||||
unitOfMeasurePrompt: "Ndi mlingo wanji (kuyeza kwa mtengo) mukufuna kutumiza ma sats kwa {{{receiver}}}?"
|
||||
amountToSendPrompt: "Lowetsani kuchuluka kwa {{{selectedCurrencyTicker}}}{{{minimumMaximumRange}}} womwe mukufuna kutumiza kwa {{{receiver}}}:"
|
||||
mediumToSendPrompt: "Kodi mukufuna kutumiza ma sats kuti:"
|
||||
noPastRecipients: "Palibe omwe adalandilapo mndandanda wanu. Chonde lowetsani wolandila kudzera pa nambala ya foni, adilesi ya lightning, kapena dzina la ogwiritsa ntchito."
|
||||
selectPastRecipient: "Sankhani {{{quickRecipientMethodText}}}:"
|
||||
recipientNotFound: "Sitinapeze wolandila"
|
||||
enterDomainForLightningAddress: "Chonde lowetsani dzina la domain kuti mumalize adilesi ya lightning yomwe imayamba ndi {{{username}}} kutumiza Bitcoin:"
|
||||
failedToUnderstandInputs: "Pepani, sitingathe kumvetsetsa zomwe zalembedwa. Chonde yesaninso."
|
||||
enterDomainForLightningAddress: "Chonde lowetsani dzina la domain kuti mumalize adilesi ya lightning yomwe imayamba ndi {{{username}}} kuti mutumize Bitcoin:"
|
||||
failedToUnderstandInputs: "Pepani, sitingathe kumvetsetsa zomwe zalembedwa. Chonde yeseraninso."
|
||||
yourLightningAddressIs: "Adilesi yanu ya lightning ndi {{{lightningAddress}}}"
|
||||
redeemBTC: "Bwezerani BTC"
|
||||
redeemBTC: "Wombolani BTC"
|
||||
whatIsALightningAddress: "Kodi adilesi ya lightning ndi chiyani?"
|
||||
getQRCode: "QR code yokhazikika"
|
||||
getOnchainAddress: "Adilesi ya Onchain"
|
||||
@ -107,120 +107,121 @@ yourQRCodeIs: "Tsamba lanu la QR code la adilesi yanu ya lightning ndi"
|
||||
bitcoinOnchain: "Bitcoin Onchain (Beta)"
|
||||
onchainRecommendations: "Malangizo a Onchain"
|
||||
shareOnchainOnce: "Chonde gawani ndikugwiritsa ntchito adilesi ya onchain kamodzi."
|
||||
addressesCanBeTracked: "Munthu aliyense amene mumagawana naye angathe kutsata malonda onse omwe amatumizidwa kwa iwo kwamuyaya."
|
||||
addressesCanBeTracked: "Munthu aliyense amene mwampatsa angathe kutsata ma transaction onse omwe amatumizidwa kwa iyo kwa nthawi zonse."
|
||||
yourBitcoinAddressIs: "Adilesi yanu ya Bitcoin ndi:"
|
||||
smsOnchainAddress: "SMS onchain adilesi"
|
||||
getNewOnchainAddress: "Pezani adilesi yatsopano ya onchain"
|
||||
newOnchainAddressAsFollows: "Adilesi yanu yatsopano ya Bitcoin onchain ndi monga pansipa:"
|
||||
newOnchainAddressAsFollows: "Adilesi yanu yatsopano ya Bitcoin onchain ili pansipa:"
|
||||
youWillReceiveSMS: "Mudzalandira kudzera ku SMS ngati malire alola."
|
||||
failedToGenerateOnchainAddress: "Sikunatheke kupanga adilesi yatsopano ya onchain. Chonde yesaninso."
|
||||
smsHasBeenSent: "SMS yatengedwa kwa adilesi:"
|
||||
checkInbox: "Chonde yang'anani m'bokosi lanu."
|
||||
generateNewAddress: "Chonde pangani adilesi yatsopano. Yomwe idakali yagwiritsidwa ntchito."
|
||||
failedToGenerateOnchainAddress: "Sizinatheke kupanga adilesi yatsopano ya onchain. Chonde yeseraninso."
|
||||
smsHasBeenSent: "SMS ya adilesi yatumizidwa:"
|
||||
checkInbox: "Chonde yang'anani m'bokosi lanu la SMS."
|
||||
generateNewAddress: "Chonde pangani adilesi yatsopano. Yakaleyi yagwiritsidwa kale ntchito."
|
||||
enterPin4AccountDetails: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti muwone zambiri za akaunti yanu:"
|
||||
machankuraBalance: "Mulingo ndi {{{balance}}} {{{currencyTicker}}} (kuyerekeza kuti ili pafupi ndi {{{fiatAmount}}} {{{fiatCurrency}}})."
|
||||
transactionHistory: "Malonda"
|
||||
purchasedVoucher: "Wogula Voucher"
|
||||
unknown: "Sadziwika"
|
||||
transactionDetail: "Mumapereka kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} {{{counterPartyText}}} (udindo: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
|
||||
machankuraBalance: "Ndalama zotsala ndi {{{balance}}} {{{currencyTicker}}} (pafupifupi {{{fiatAmount}}} {{{fiatCurrency}}})."
|
||||
transactionHistory: "ma transaction"
|
||||
purchasedVoucher: "Voucher yogulidwa"
|
||||
unknown: "Zosadziwika"
|
||||
transactionDetail: "Mwatumiza kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} {{{counterPartyText}}} (womwe zilili: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
|
||||
electricity: "Magetsi"
|
||||
electricityTransactionDetail: "Mumapereka kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} Lightning Watts (udindo: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
|
||||
failedToProcess: "Sikunatheke kugwira ntchito malondawo."
|
||||
noTransaction: "Simunachitepo ntchito ndi Machankura. Zimenezi zisintha mukatumiza kapena kulandira Bitcoin pogwiritsa ntchito Machankura."
|
||||
electricityTransactionDetail: "Mwatumiza kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} Lightning Watts (momwe zilili: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
|
||||
failedToProcess: "Sizinatheke."
|
||||
noTransaction: "Simunatumizepo kapena kulandira pa Machankura. Zimenezi zisintha mukatumiza kapena kulandira Bitcoin pogwiritsa ntchito Machankura."
|
||||
select: "Sankhani:"
|
||||
more: "zambiri"
|
||||
failedTransactionHistory: "Sikunatheke kufotokozera mbiri yamalonda."
|
||||
failedTransactionHistory: "Sizinatheke kupereka mbiri ya akaunti."
|
||||
buyUsingMachankura: "Gulani pogwiritsa ntchito Machankura"
|
||||
integrationComingSoon: "Kulumikizana kuti mugwiritse ntchito BTC kukubwera posachedwa."
|
||||
buyAirtime: "Gulani airtime:"
|
||||
buyAirtime: "Gulani mayunitsi:"
|
||||
forYourNumber: "Nambala yanu ({{{phoneNumber}}})"
|
||||
forAnotherNumber: "Kwa nambala ina"
|
||||
enterPhoneNumberForAirtime: "Lowetsani nambala ya foni yomwe mukufuna kugula airtime:"
|
||||
pickAProduct: "Sankhani chinthu"
|
||||
yourself: "inu nokha"
|
||||
failedAirtimePinProduct: "Sikunatheke kugwira ntchito airtime pin product."
|
||||
forAnotherNumber: "Ku nambala ina"
|
||||
enterPhoneNumberForAirtime: "Lowetsani nambala ya foni yomwe mukufuna kugula mayunitsi:"
|
||||
pickAProduct: "Sankhani katundu"
|
||||
yourself: "inu eni"
|
||||
failedAirtimePinProduct: "Sizinatheke kupanga pin ya mayunitsi."
|
||||
enterWattsMeterNumber: "Chonde lowetsani nambala ya mita yomwe mukufuna kugula magetsi:"
|
||||
enterWattsAmount: "Chonde lowetsani kuchuluka kwa magetsi omwe mukufuna kugula (osachepera: 25 ZAR, osapitilira: 1 000 ZAR):"
|
||||
enterPinForWatts: "Chonde lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{satoshis}}} sats ({{{zarAmount}}} ZAR) kwa {{{meterNumberInput}}}:"
|
||||
failedWattsPurchase: "Sikunatheke kupeza invoice kuti mugule magetsi kwa nambala ya mita {{{meterNumberInput}}}. Chonde yesaninso."
|
||||
initiatedWattsPurchase: "Mwayambitsa kugula {{{amountInSatoshis}}} sats ({{{amountInZAR}}} ZAR) kuti mugule magetsi kwa {{{meterNumber}}}."
|
||||
failedWattsPurchaseWithAmount: "Sikunatheke kuyambitsa kugula {{{amountInZAR}}} ZAR wa magetsi kwa {{{meterNumberInput}}} ku Machankura. Chonde yesaninso."
|
||||
enterPinForWatts: "Chonde lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{satoshis}}} sats ({{{zarAmount}}} ZAR) ku {{{meterNumberInput}}}:"
|
||||
failedWattsPurchase: "Sizinatheke kupeza invoice kuti mugule magetsi ku nambala ya mita {{{meterNumberInput}}}. Chonde yeseraninso."
|
||||
initiatedWattsPurchase: "Ntchito yogula {{{amountInSatoshis}}} sats ({{{amountInZAR}}} ZAR) kuti mugule magetsi ku {{{meterNumber}}}."
|
||||
failedWattsPurchaseWithAmount: "Sizinatheke kuyamba kugula {{{amountInZAR}}} ZAR wa magetsi ku {{{meterNumberInput}}} ku Machankura. Chonde yeseraninso."
|
||||
wattsValidRangePrompt: "Chonde lowetsani nambala pakati pa 25 ZAR ndi 1000 ZAR."
|
||||
wattsInvalidMeterNumber: "Nambala ya mita yomwe mwalemba siyolondola. Chonde yesaninso."
|
||||
wattsInvalidMeterNumber: "Nambala ya mita yomwe mwalemba siyolondola. Chonde yeseraninso."
|
||||
pickElectricityVendor: "Sankhani wogulitsa magetsi"
|
||||
pickPetrolGarage: "Sankhani gareji ya petrol"
|
||||
pickPetrolGarage: "Sankhani filing station/Malo omwetsera mafuta"
|
||||
pickAStore: "Sankhani sitolo"
|
||||
categoryInactive: "Chigawo sichinakhalepo. Chonde yesaninso pambuyo pake."
|
||||
btcExchangeRate: "BTC mtengo wosinthira"
|
||||
categoryInactive: "Gawo ili silinakhazikitsidwe. Chonde yeseraninso nthawi ina."
|
||||
btcExchangeRate: "Mtengo wosinthira BTC"
|
||||
bitcoin: "Bitcoin"
|
||||
thankYouForVisiting: "Zikomo chifukwa chobwera ku Machankura."
|
||||
welcomeToMachankura: "Takulandirani ku Machankura (chikwama cha Bitcoin pa foni)"
|
||||
thankYouForVisiting: "Zikomo posankha Machankura."
|
||||
welcomeToMachankura: "Takulandirani ku Machankura (Wallet ya Bitcoin pa foni)"
|
||||
welcomeToMachankuraShort: "Takulandirani ku Machankura"
|
||||
whatYouWantPrompt: "Mukufuna kuchita chiyani"
|
||||
registerAccount: "Lowetsani akaunti"
|
||||
changeLanguage: "Sinthani Chilankhulo"
|
||||
machankuraIsAMobileService: "Machankura ndi ntchito ya m'manja yomwe imatumiza ndikulandira Bitcoin m’malo mwanu kudzera pa nambala ya foni yanu."
|
||||
whatYouWantPrompt: "Zomwe mukufuna kuchita"
|
||||
registerAccount: "Tsegulani akaunti"
|
||||
changeLanguage: "Sinthani Chiyankhulo"
|
||||
machankuraIsAMobileService: "Machankura ndi ntchito yapafoni ya m'manja yomwe imatumiza ndikulandira Bitcoin m’malo mwanu kudzera pa nambala ya foni yanu."
|
||||
learnAboutBitcoin: "Phunzirani za Bitcoin"
|
||||
bitcoinIsElectronicMoney: "Bitcoin ndi ndalama zamagetsi zamagulu osiyanasiyana zomwe zinayambitsidwa ndi Satoshi Nakamoto mu 2008. Ndi ndalama zokhazokha zapaintaneti."
|
||||
thankYouForVisitingTillNextTime: "Zikomo chifukwa cha kuyesa Machankura. Tidzakhala okondwa kukuthandizani mukabweranso nthawi ina."
|
||||
registerAccountPrompt: "Kuti mupange akaunti ya Machankura, chonde lowetsani PIN ya 5-digit yomwe mudzagwiritse ntchito mukamagwiritsa ntchito akaunti yanu:"
|
||||
bitcoinIsElectronicMoney: "Bitcoin ndi ndalama zotumizidwa Ndi kulandiridwa ndi mphamvu yamagetsi zogwiritsidwa zoyendetsedwa Ndi kugwiritsidwa nthchito ndi wina aliyense, kwina kulikonse, nthawi iliyonse, zomwe zinayambitsidwa ndi Satoshi Nakamoto mu 2008. Ndi ndalama zokhazokha zapaintaneti."
|
||||
thankYouForVisitingTillNextTime: "Zikomo posankha Machankura. Tidzakhala okondwa kukuthandizani mukabweranso nthawi ina."
|
||||
registerAccountPrompt: "Kuti mutsegule akaunti ya Machankura, chonde lowetsani PIN ya zilembo 5 (5-digit) yomwe kumagwiritsa ntchito ntchito akaunti yanu:"
|
||||
youHaveGifts: "Muli ndi mphatso {{{giftCount}}} zomwe zikukuyembekezerani ;) (pitani ku Menyu ndikuwona zambiri za akaunti)."
|
||||
enjoySendingAndReceiving: "Sangalalani kutumiza ndi kulandira Bitcoin. ;)"
|
||||
accountCreated: "Tapanga akaunti yanu ya Machankura."
|
||||
failedToCreateUser: "Sikunatheke kupanga wogwiritsa ntchito. Chonde yesaninso."
|
||||
failedToCreateUser: "Sizinatheke kupanga wogwiritsa ntchito. Chonde yeseraninso."
|
||||
englishOnly: "Chingerezi ndiye chilankhulo chokha chomwe chilipo ku Machankura pakadali pano. Tikuwonjezera zambiri posachedwa."
|
||||
exchangeBTC: "Sinthani BTC"
|
||||
clans: "Mabanja"
|
||||
clans: "Magulu"
|
||||
back: "Kubwerera"
|
||||
enterSendMediumPrompt: "Chonde lowetsani {{{medium}}} kuti mutumize Bitcoin:"
|
||||
lightningInvoice: "LN Invoice (Bolt11)"
|
||||
onchain: "Onchain"
|
||||
lightningInvoicesUnsupported: "Pepani, ma LN Invoice sathandizidwa kudzera ku USSD chifukwa nthawi zambiri amakhala otalikirapo kuti agwirizane ndi malire a zilembo 160 za USSD."
|
||||
lightningInvoicesUnsupported: "Pepani, ma LN Invoice palibe kudzera ku USSD chifukwa nthawi zambiri amakhala otalikirapo kuti agwirizane ndi malire a zilembo 160 za USSD."
|
||||
minimumMaximumRange: "(Osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, Osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})"
|
||||
amountConversionText: "({{{amountInSats}}} sats = {{{amountConverted}}} {{{convertedCurrencyTicker}}})"
|
||||
sendBitcoinConfirmation: "Muli pafupi kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} (chindapusa cha ntchito: {{{feeText}}}{{{networkFeeText}}})."
|
||||
networkFee: "chindapusa cha netiweki: {{{networkFeeText}}} ${currencyTicker}"
|
||||
sendSats: "Tumizani sats"
|
||||
sendBitcoinConfirmation: "Muli pafupi kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} (mtengo wake: {{{feeText}}}{{{networkFeeText}}})."
|
||||
networkFee: "mtengo wa netiweki: {{{networkFeeText}}} ${currencyTicker}"
|
||||
sendSats: "Tumizani ma sats"
|
||||
pleaseUseWebForBolt11: "Chonde gwiritsani ntchito tsamba lawebusayiti pansipa kuti mupange (Bolt 11) Lightning Invoice ndikulandira sats ku akaunti yanu."
|
||||
lightningInvoiceShort: "LN Invoice"
|
||||
languages: "Zilankhulo"
|
||||
noOtherLanguagesAvailable: "Palibe zilankhulo zina zomwe zilipo."
|
||||
changeLanguageExplanation: "Mukangosintha izi, mawu onse omwe mudzawona ku Machankura azikhala mChichewa."
|
||||
changeLanguagePinPrompt: "Lowetsani {{pin}} kuti musinthe chilankhulo kukhala Chichewa"
|
||||
changeLanguageConfirmation: "Sinthani chilankhulo kukhala Chichewa"
|
||||
changeLanguageConfirmation: "Sinthani chiyankhulo kukhala Chichewa"
|
||||
cancel: "Letsani"
|
||||
changeLanguageSuccessful: "Chilankhulo chogwiritsidwa ntchito ku Machankura chasinthidwa kukhala Chingerezi."
|
||||
changeLanguageFailed: "Sizinatheke kusintha chilankhulo chomwe mukufuna. Chonde yeseraninso."
|
||||
cancel: "Letsani"
|
||||
changeLanguageSuccessful: "Chilankhulo chomwe chimagwiritsidwa ntchito ku Machankura chasinthidwa kukhala Chingerezi."
|
||||
changeLanguageFailed: "Sikunatheke kusintha zokonda chilankhulo chomwe mukufuna. Chonde yesaninso."
|
||||
account: "Akaunti"
|
||||
security: "Chitetezo"
|
||||
noPastElectricityMeters: "Palibe manambala a mita zakale"
|
||||
thankYouForVisitingReturnToCreateAccount: "Zikomo potipatsa mwayi ku Machankura. Chonde bwererani kuti mupange akaunti."
|
||||
noPastElectricityMeters: "Palibe manambala akale a mita"
|
||||
thankYouForVisitingReturnToCreateAccount: "Zikomo posankha Machankura. Chonde bwererani kuti mutsegule akaunti."
|
||||
machankuraSecurityManagement: "Kusamalira Chitetezo cha Machankura:"
|
||||
accessLock: "Kutsekereza Mwayi (kufunika PIN pa ntchito)"
|
||||
accessLock: "Chitetezo (kufunika PIN pa ntchito)"
|
||||
managePIN: "Sinthani PIN"
|
||||
manageAuthenticatorOTP: "Sinthani Wotsimikizira OTP"
|
||||
configureAuthenticatorOTP: "Sinthani Makonzedwe a Wotsimikizira OTP"
|
||||
manageAuthenticatorOTP: "Sinthani ndondomeko yotsimikizira OTP"
|
||||
configureAuthenticatorOTP: "Ikani ndondomeko yotsimikizira OTP"
|
||||
authenticatorOTP: "OTP ya Wotsimikizira"
|
||||
lockAccess: "Tsekani Mwayi"
|
||||
lockRequiredExplanation: "Kufunika kulowetsa PIN/OTP kuti mupeze sats"
|
||||
lockNotRequiredExplanation: "Mungapeze sats popanda kulowetsa PIN/OTP"
|
||||
disableLock: "Zimitsani Kutsekereza"
|
||||
enableLock: "Yambitsani Kutsekereza"
|
||||
accessLockHasBeenEnabled: "Kutsekereza kwapangidwa."
|
||||
accessLockHasBeenDisabled: "Kutsekereza kwachotsedwa."
|
||||
disableLock: "Chotsani chitetezo"
|
||||
enableLock: "Ikani chitetezo"
|
||||
accessLockHasBeenEnabled: "Chitetezo chaikidwa."
|
||||
accessLockHasBeenDisabled: "Chitetezo chachotsedwa."
|
||||
yourMachankura: "Yanu"
|
||||
securityMechanism: "{{{your}}} {{{pinOrOTP}}}"
|
||||
accessLockHasBeenEnabledExplanation: "Tsopano muyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti mupeze sats."
|
||||
accessLockHasBeenEnabledExplanation: "Tsopano muyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti muone sats."
|
||||
accessLockHasBeenDisabledExplanation: "Tsopano simuyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti mupeze sats."
|
||||
enterLockMechanismToSetUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti mukhazikitse dzina la wosuta pa adilesi yanu ya mphezi:"
|
||||
enterLockMechanismToSetUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti mukhazikitse dzina la wogwirista nthchito pa adilesi yanu ya lightning:"
|
||||
enterLockMechanismToUpdateUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti musinthe dzina la wosuta la adilesi yanu ya mphezi:"
|
||||
accountSettings: "Zokonzekera Akaunti"
|
||||
accountSettings: "Zothandizira Akaunti"
|
||||
deleteAccount: "Chotsani Akaunti"
|
||||
yourAboutToRequestAccountDelete: "Mukukonzekera kupempha kuchotsa akaunti yanu kwamuyaya:"
|
||||
cancelledDeletingAccount: "Mwasiya njira yochotsa akaunti yanu. Zikomo potipitilira ndi Machankura."
|
||||
deleteAccountConsequences: "Mgwirizano wonse ndi deta ya malonda ndi dongosolo yomwe ikukhudzana ndi akaunti yanu ichotsedwa:"
|
||||
deleteAccountRequestSubmitted: "Pempho lanu lochotsa akaunti lawunikidwa. Mudzalandira zosintha zikamalizidwa."
|
||||
failedToSubmitDeleteAccountRequest: "Pempho lanu lochotsa akaunti lachotsedwa."
|
||||
yourAboutToRequestAccountDelete: "Mukukonzekera kupempha kuchotsa akaunti yanu kwa nthawi zonse:"
|
||||
cancelledDeletingAccount: "Mwasiya nthchito yochotsa akaunti yanu. Zikomo potipitilira ndi Machankura."
|
||||
deleteAccountConsequences: "Mgwirizano wonse ndi mbiri ya ma transaction ndi dongosolo lomwe ikukhudzana ndi akaunti yanu ichotsedwa:"
|
||||
deleteAccountRequestSubmitted: "Pempho lanu lochotsa akaunti laperekedwa. Mudzalandira zosintha zikamalizidwa."
|
||||
failedToSubmitDeleteAccountRequest: "Pempho lanu lochotsa akaunti silinaperekedwe."
|
||||
deleteAccountTODO: "Ntchito yochotsa akaunti siyinathe."
|
||||
functionalityComingSoon: "Ntchito ikubwera posachedwa."
|
||||
createAccountExplanation: "Mukakhazikitsa akaunti ya Machankura, mutha kutumiza ndi kulandira Bitcoin:"
|
||||
|
Loading…
x
Reference in New Issue
Block a user