Edited Chichewa languages

This commit is contained in:
kngako 2024-05-11 22:27:19 +02:00
parent acca2f4055
commit 785b9086dd

View File

@ -1,103 +1,103 @@
welcomeHeading: "Takulandirani ku Machankura" welcomeHeading: "Takulandirani ku Machankura"
productAmountPrompt: "Kodi mugula ndalama zingati za {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} kwa {{{recipient}}}" productAmountPrompt: "Kodi mugula {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} ochuluka bwanji kwa {{{recipient}}}"
amountRangeText: "(osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})" amountRangeText: "(osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})"
inCurrencyPrompt: "(mu {{{currencyTicker}}})" inCurrencyPrompt: "(mu {{{currencyTicker}}})"
inputAmountOutOfRangePrompt: "Simungathe kugula ma airtime kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa" inputAmountOutOfRangePrompt: "Simungathe kugula ma yunitsi kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa"
inputAmountOutOfRangeProductPrompt: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa" inputAmountOutOfRangeProductPrompt: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} kunja kwa malire amene adakhazikitsidwa"
pleaseTryAgain: "Chonde yesaninso." pleaseTryAgain: "Chonde yeseraninso."
menu: "Menyu" menu: "Menyu"
inputAmountImpossible: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} ndi zolemba zomwe zilipo {{{amountInput}}}" inputAmountImpossible: "Simungathe kugula {{{bitrefillProductName}}} ndi zolembedwazi {{{amountInput}}}"
enterMachankuraPinForAirtime: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{inputAmountValue}}} {{{productCurrencyTicker}}} ({{{btcAmount}}} {{{currencyTicker}}}) {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} kwa {{{phoneNumber}}}" enterMachankuraPinForAirtime: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{inputAmountValue}}} {{{productCurrencyTicker}}} ({{{btcAmount}}} {{{currencyTicker}}}) {{{bitrefillProductName}}} {{{categoryType}}} kwa {{{phoneNumber}}}"
failedToConfirmAction: "Sikunakwanitse kutsimikizira zomwe mwachita. Chonde yesaninso." failedToConfirmAction: "Simunakwanitse kutsimikizira zomwe mwachita. Chonde yeseraninso."
inputAmountInvalid: "Ndalama sizikugwirizana. Chonde yesaninso." inputAmountInvalid: "Ndalama sizikugwirizana. Chonde yeseraninso."
productPurchaseInitiated: "Mwayambitsa kugula {{{categoryType}}}. Onani mbiri ya malonda kuti mumve zambiri." productPurchaseInitiated: "Kugula kwayambika." {{{categoryType}}}. Onani ma transaction kuti mudziwe zambiri."
productPurchaseFailed: "Kugula {{{categoryType}}} kunalephera. Chonde yesaninso." productPurchaseFailed: "Kugula {{{categoryType}}} kwalephereka. Chonde yeseraninso."
yourPhoneNumberNotSupported: "Nambala yanu ya foni {{{airtimeReceipent}}} panopa ilibe zinthu zomwe tingathandize kubereka." yourPhoneNumberNotSupported: "Nambala yanu ya foni {{{airtimeReceipent}}} panopa ilibe zinthu zomwe tingathandize kupereka."
pinDontMatch: "PIN yanu ya Machankura siyikugwirizana ndi PIN yomwe ili mu dongosolo lathu. Chonde yesaninso." pinDontMatch: "PIN yanu ya Machankura siyikugwirizana ndi PIN yomwe ili mu dongosolo lathu. Chonde yeseraninso."
balanceTooLow: "Mulingo wanu wa ndalama ndi wochepa kwambiri kuti muchite izi. Chonde yesaninso." balanceTooLow: "Ndalama zanu zotsala ndi zochepa kwambiri kuti muchite izi. Chonde yeseraninso."
purchaseFailed: "Sikunatheke kugula. Chonde yesaninso." purchaseFailed: "Sizinatheke kugula. Chonde yeseraninso."
phoneNumberNotSupported: "Nambala ya foni siyikugwirizana. Chonde yesaninso." phoneNumberNotSupported: "Nambala ya foni siyikugwirizana. Chonde yeseraninso."
pickYourNetwork: "Sankhani netiweki yanu" pickYourNetwork: "Sankhani netiweki yanu"
pickNetworkFailure: "Sitinatheke kugwira ntchito yosankha netiweki. Chonde yesaninso." pickNetworkFailure: "Sizinatheke kusankha netiweki. Chonde yeseraninso."
phoneNumber: "Nambala ya Foni" phoneNumber: "Nambala ya Foni"
lightningAddress: "Adilesi ya Lightning" lightningAddress: "Adilesi ya Lightning"
lightningAddressPrompt: "(Kwa wolemba pang'onopang'ono, ingolemba dzina la ogwiritsa ntchito ndipo patsamba lotsatira lowetsani domain)" lightningAddressPrompt: "(Kwa wolemba pang'onopang'ono, ingolembani dzina la ogwiritsa ntchito ndipo patsamba lotsatira lowetsani domain)"
machankuraUsername: "Dzina la ogwiritsa ntchito" machankuraUsername: "Dzina la ogwiritsa ntchito"
unsupported: "sizikuthandizidwa" unsupported: "pakanalibe"
mostRecent: "Zaposachedwa Kwambiri" mostRecent: "Zongochitika posachedwa"
mostFrequent: "Zomwe Zimachitika Kawirikawiri" mostFrequent: "Zochitika kawirikawiri"
inputReceipentToBuy: "Chonde lowetsani {{{recipientText}}} yemwe mukufuna kugula {{{bitrefillProductName}}} kwa:" inputReceipentToBuy: "Chonde lowetsani {{{recipientText}}} yemwe mukufuna kugula {{{bitrefillProductName}}} kwa:"
vendorNotFound: "Sitinapeze wogulitsa malinga ndi zomwe mwalemba. Chonde yesaninso." vendorNotFound: "Sitinapeze wogulitsa malinga ndi zomwe mwalemba. Chonde yeseraninso."
enterPinToSend: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mutumize {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}:" enterPinToSend: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mutumize {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}:"
lowBalancePleaseIncrease: "Mulingo wanu wa ndalama ({{{balance}}} {{{currencyTicker}}}) ndi wochepa kwambiri. Onjezerani ndalama kapena mutumize zochulukirapo kuposa {{{amountText}}}" lowBalancePleaseIncrease: "Ndalama zanu zotsala ({{{balance}}} {{{currencyTicker}}}) ndi zochepa kwambiri. Onjezerani ndalama zotsala kapena mutumize zocheperapo zosapitilira {{{amountText}}}"
cannotSendToYourself: "Simungathe kutumiza ndalama kwa inu nokha. Chonde yesaninso ndi wolandila wina." cannotSendToYourself: "Simungathe kudzitumizira ndalama nokha. Chonde yeseraninso kutumizira wina."
successfullySent: "Mwatumiza bwino {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}." successfullySent: "Mwakwanitsa kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}."
failedToSend: "Sikunatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso." failedToSend: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso."
successfullyGiftedSats: "Mwathandizira {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Ali ndi masiku 21 kuti apeze mphatso yanu, chonde muwauze kuti ayambe akaunti ya Machankura." successfullyGiftedSats: "Mwakwanitsa kugawa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Ali ndi masiku 21 kuti alandire mphatso yanu. Chonde auzeni kuti atsegule akaunti ya Machankura poimba mwaulere *384*8333*0265#."
failedToGiftSats: "Sikunatheke kuthandiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso ndi mitengo ina." failedToGiftSats: "Sizinatheke kugawa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso ndi mlingo wina."
giftCountryUnsupported: "Simungathebe kugawa Bitcoins kwa nambala za foni m'mayiko amenewo." giftCountryUnsupported: "Simungathe kugawa ma Bitcoin kwa manambala za foni m'dziko limenelo."
failedTransfer: "Sikunatheke kusamutsa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso." failedTransfer: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso."
initiatedTransfer: "Kutumiza kwanu kwa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} kwayamba. Onani ma transaction anu kuti mudziwe zambiri." initiatedTransfer: "Kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} kwayambika. Onani ma transaction anu kuti mudziwe zambiri."
failedTransferLightningAddress: "Sikunatheke kusamutsa {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yesaninso kapena adilesi ina ya lightning." failedTransferLightningAddress: "Sizinatheke kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}}. Chonde yeseraninso kapena tumizani ku adilesi ina ya lightning."
lowBalanceForServiceFeePleaseIncrease: "Mulingo wanu wa ndalama ({{{satsBalance}}} sats) ndi wochepa kwambiri kuti mupereke chindapusa cha ntchito ({{{feeText}}}). Onjezerani ndalama kapena mutumize zocheperako kuposa {{{amountText}}}" lowBalanceForServiceFeePleaseIncrease: "Ndalama zanu ({{{satsBalance}}} sats) ndi zochepa kwambiri ({{{feeText}}}). Chonde onjezerani ndalama kapena tumizani zocheperako, zosapitilira {{{amountText}}}"
aztecoVoucherAlreadyRedeemed: "Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) idakali yobwezeretsedwa." aztecoVoucherAlreadyRedeemed: "Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) yawomboledwa kale."
redeemAztecoVoucherPrompt: "Tikukonzekera kubweza Azteco voucher wamtengo wa {{{satsAmount}}} sats ku akaunti yanu ya Machankura." redeemAztecoVoucherPrompt: "Tikukonzekera kuwombola Azteco voucher yamtengo wa {{{satsAmount}}} sats ku akaunti yanu ya Machankura."
redeem: "Bwezerani" redeem: "Wombolani"
decline: "Kukana" decline: "Letsani"
failedToRedeemAztecoVoucher: "Sikunatheke kubweza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso." failedToRedeemAztecoVoucher: "Sizinatheke kuwombola Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
failedToProcessAztecoVoucher: "Sikunatheke kukonza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso." failedToProcessAztecoVoucher: "Sizinatheke kukonza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
failedToAccessAztecoVoucher: "Sikunatheke kupeza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yesaninso." failedToAccessAztecoVoucher: "Sizinatheke kupeza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) chifukwa cha zolakwika zamkati. Chonde yeseraninso."
initiatedAztecoOnchainRedemption: "Mwayambitsa kubwezera. Azteco onchain voucher akubweza." initiatedAztecoOnchainRedemption: "Mwayamba kuwombola. Azteco onchain voucher ikuwomboledwa."
errorGeneratingOnchainAddress: "Cholakwika chamkati pakupanga adilesi. Chonde yesaninso." errorGeneratingOnchainAddress: "Kupanga address kwakanika. Chonde yeseraninso."
redemptionInProgress: "Kubwezera kukuyenda. Chonde dikirani." redemptionInProgress: "Ntchito yowombola ilim'kati. Chonde dikirani."
reattemptAztecoRedemptionTitle: "Mwayesanso kubwezera" reattemptAztecoRedemptionTitle: "Mukuyeseranso kuwombola"
reattemptAztecoRedemptionBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) akubwezera Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri." reattemptAztecoRedemptionBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) ikuwombola Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
redeem1ForYouTitle: "Mwayambitsa kubwezera" redeem1ForYouTitle: "Mwayamba kuwombola"
redeem1ForYouBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) akubwezera Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri." redeem1ForYouBody: "1 For You voucher ({{{aztecoVoucherCode}}}) ikuwombola Bitcoin kudzera ku Azteco. Chonde dikirani kuti mumve zambiri."
successfullyInitiatedRedemption: "Mwayambitsa bwino kubwezera kwa Azteco voucher (mudzalandira {{{amountInSatoshis}}} sats). Mudzalandira zatsopano zokhudzana ndi kusamutsa." successfullyInitiatedRedemption: "Mwakwanitsa kayamba kuwombola Azteco voucher (mudzalandira {{{amountInSatoshis}}} sats). Mulandira zotsatira."
failedToFindAztecoVoucher: "Sikunatheke kupeza Azteco voucher {{{aztecoVoucherCode}}}" failedToFindAztecoVoucher: "Sizinatheke kupeza Azteco voucher {{{aztecoVoucherCode}}}"
declinedRedemption: "Mwakana kubweza Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}})." declinedRedemption: "Mwakana kuwombola Azteco voucher ({{{aztecoVoucherCode}}})."
sendBTC: "Tumizani BTC" sendBTC: "Tumizani BTC"
receiveBTC: "Landirani BTC" receiveBTC: "Landirani BTC"
balanceAndHistory: "Mulingo ndi zambiri" balanceAndHistory: "Ndalama zotsala komanso zambiri"
barterBTC: "Barter Goods/Services" barterBTC: "Kugula katundu/kulipira"
settings: "Zokonda" settings: "Zothandizira"
exit: "Tulukani" exit: "Tulukani"
username: "Dzina la ogwiritsa ntchito" username: "Dzina la ogwiritsa ntchito"
pin: "PIN" pin: "PIN/ nambala ya chinsinsi"
language: "Chilankhulo" language: "Chiyankhulo"
learnMore: "Phunzirani zambiri" learnMore: "Phunzirani zambiri"
enterPinToUpdateUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti musinthe dzina lanu la ogwiritsa ntchito la adilesi ya lightning" enterPinToUpdateUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti musinthe dzina lanu la ogwiritsa ntchito la address ya lightning"
enterPinToSetUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mukhazikitse dzina la ogwiritsa ntchito la adilesi yanu ya lightning:" enterPinToSetUsername: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti muyike dzina la ogwiritsa ntchito la adilesi yanu ya lightning:"
enterUsername: "Lowetsani malemba omwe mukufuna monga dzina lanu latsopano la ogwiritsa ntchito:" enterUsername: "Sankhani dzina lomwe mukufuna kukhala dzina lanu latsopano la ogwiritsa ntchito:"
usernameUpdated: "Dzina lanu la ogwiritsa ntchito lasinthidwa kukhala {{{proposedUsernameText}}}. Adilesi yanu ya lightning tsopano ndi {{{proposedUsernameText}}}@{{{domain}}}." usernameUpdated: "Dzina lanu la ogwiritsa ntchito lasinthidwa kukhala {{{proposedUsernameText}}}. Address yanu ya lightning tsopano ndi {{{proposedUsernameText}}}@{{{domain}}}."
enterDifferentUsername: "Sikugwirizana kusintha dzina la ogwiritsa ntchito. Chonde lowetsani dzina lina la ogwiritsa ntchito ({{{proposedUsernameText}}} ndi {{{errorStatus}}}):" enterDifferentUsername: "Sizinatheke kusintha dzina la ogwiritsa ntchito. Chonde lowetsani dzina lina ({{{proposedUsernameText}}} ndi {{{errorStatus}}}):"
languageSettingsComingSoon: "Zokonda zilankhulo zikubwera posachedwa." languageSettingsComingSoon: "Zosintha chiyankhulo zikubwera posachedwa."
learnMoreSettingsComingSoon: "Zokonda zophunzirira zambiri zikubwera posachedwa." learnMoreSettingsComingSoon: "Zokhudza kuphunzirira zambiri, zikubwera posachedwa."
resetPinCountDown: "Mudzatha kukonzanso PIN yanu kuchokera {{{when}}} tsopano. Chonde bwerani patsamba lino pambuyo pake." resetPinCountDown: "Mudzatha kusintha PIN yanu kuchokera {{{when}}} tsopano. Chonde bwerani patsamba lino pambuyo pake."
cancelPinReset: "Kuti mubwezere kubwezeretsa PIN, lowetsani PIN yanu yamakono" cancelPinReset: "Kuti muletse kubwezeretsa PIN, lowetsani PIN yanu ya Machankura"
cancelledPinReset: "Pempho lanu lobwezeretsa PIN layimitsidwa. Zikomo pogwiritsa ntchito Machankura." cancelledPinReset: "Pempho lanu lobwezeretsa PIN layimitsidwa. Zikomo pogwiritsa ntchito Machankura."
pinUpdated: "PIN yanu ya Machankura yasinthidwa kukhala yomwe mwangoyiyika." pinUpdated: "PIN yanu ya Machankura yasinthidwa kukhala yomwe mwangoyiyika."
enterNewPin: "Lowetsani PIN yanu yatsopano yamakilogalamu 5:" enterNewPin: "Lowetsani PIN yanu yatsopano yazilembo 5:"
expiredPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwatha. Yesaninso." expiredPinReset: "Nthawi yosinthira PIN yadutsa. Chonde yeseraninso."
pinManagement: "Kasamalidwe ka PIN ya Machankura" pinManagement: "Kasamalidwe ka PIN ya Machankura"
changePin: "Sinthani PIN" changePin: "Sinthani PIN"
resetPin: "Kubwezeretsa PIN (muiwala PIN)" resetPin: "Kubwezeretsa PIN (muiwala PIN)"
resetPinPrompt: "Kuti mubwezeretse PIN yanu (chifukwa mwaiwala PIN yanu), muyenera kuyambitsa ndondomeko ya maola 24 (imatha maola 48)." resetPinPrompt: "Kuti mubwezeretse PIN yanu (chifukwa mwaiwala PIN yanu), muyenera kuyamba ndondomeko yosinthira ya maola 24 (imatha maola 48)."
startPasswordReset: "Yambani kubwezeretsa mawu achinsinsi" startPasswordReset: "Yambani kubwezeretsa nambala yachinsinsi (PIN)"
initiatedPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwakhazikitsidwa. Mudzatha kukhazikitsa mawu achinsinsi atsopano m'maola 24. Kuti muyime pempho, mutha kulowa PIN yanu yamakono." initiatedPinReset: "Kubwezeretsa PIN kwakhazikitsidwa. Mudzakwanitsa kuyika nambala yachinsinsi yatsopano m'maola 24. Kuti muyimitse pempho lanu, mutha kulowa PIN yanu yamakono."
failedPinResetInitiation: "Sikunatheke kuyambitsa kubwezeretsa PIN. Chonde yesaninso." failedPinResetInitiation: "Sizinatheke kuyamba kubwezeretsa PIN. Chonde yeseraninso."
enterCurrentPin: "Lowetsani PIN yanu yamakono:" enterCurrentPin: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura yomwe mumagwiritsa nthchito:"
unitOfMeasurePrompt: "Mukatani (kuyeza kwa mtengo) mungakonde kutumiza sats kwa {{{receiver}}}?" unitOfMeasurePrompt: "Ndi mlingo wanji (kuyeza kwa mtengo) mukufuna kutumiza ma sats kwa {{{receiver}}}?"
amountToSendPrompt: "Lowetsani kuchuluka kwa {{{selectedCurrencyTicker}}}{{{minimumMaximumRange}}} komwe mukufuna kutumiza kwa {{{receiver}}}:" amountToSendPrompt: "Lowetsani kuchuluka kwa {{{selectedCurrencyTicker}}}{{{minimumMaximumRange}}} womwe mukufuna kutumiza kwa {{{receiver}}}:"
mediumToSendPrompt: "Kodi mukufuna kutumiza sats kuti:" mediumToSendPrompt: "Kodi mukufuna kutumiza ma sats kuti:"
noPastRecipients: "Palibe omwe alandila pa mndandanda. Chonde lowetsani wolandila kudzera pa nambala ya foni, adilesi ya lightning, kapena dzina la ogwiritsa ntchito." noPastRecipients: "Palibe omwe adalandilapo mndandanda wanu. Chonde lowetsani wolandila kudzera pa nambala ya foni, adilesi ya lightning, kapena dzina la ogwiritsa ntchito."
selectPastRecipient: "Sankhani {{{quickRecipientMethodText}}}:" selectPastRecipient: "Sankhani {{{quickRecipientMethodText}}}:"
recipientNotFound: "Sitinapeze wolandila" recipientNotFound: "Sitinapeze wolandila"
enterDomainForLightningAddress: "Chonde lowetsani dzina la domain kuti mumalize adilesi ya lightning yomwe imayamba ndi {{{username}}} kutumiza Bitcoin:" enterDomainForLightningAddress: "Chonde lowetsani dzina la domain kuti mumalize adilesi ya lightning yomwe imayamba ndi {{{username}}} kuti mutumize Bitcoin:"
failedToUnderstandInputs: "Pepani, sitingathe kumvetsetsa zomwe zalembedwa. Chonde yesaninso." failedToUnderstandInputs: "Pepani, sitingathe kumvetsetsa zomwe zalembedwa. Chonde yeseraninso."
yourLightningAddressIs: "Adilesi yanu ya lightning ndi {{{lightningAddress}}}" yourLightningAddressIs: "Adilesi yanu ya lightning ndi {{{lightningAddress}}}"
redeemBTC: "Bwezerani BTC" redeemBTC: "Wombolani BTC"
whatIsALightningAddress: "Kodi adilesi ya lightning ndi chiyani?" whatIsALightningAddress: "Kodi adilesi ya lightning ndi chiyani?"
getQRCode: "QR code yokhazikika" getQRCode: "QR code yokhazikika"
getOnchainAddress: "Adilesi ya Onchain" getOnchainAddress: "Adilesi ya Onchain"
@ -107,120 +107,121 @@ yourQRCodeIs: "Tsamba lanu la QR code la adilesi yanu ya lightning ndi"
bitcoinOnchain: "Bitcoin Onchain (Beta)" bitcoinOnchain: "Bitcoin Onchain (Beta)"
onchainRecommendations: "Malangizo a Onchain" onchainRecommendations: "Malangizo a Onchain"
shareOnchainOnce: "Chonde gawani ndikugwiritsa ntchito adilesi ya onchain kamodzi." shareOnchainOnce: "Chonde gawani ndikugwiritsa ntchito adilesi ya onchain kamodzi."
addressesCanBeTracked: "Munthu aliyense amene mumagawana naye angathe kutsata malonda onse omwe amatumizidwa kwa iwo kwamuyaya." addressesCanBeTracked: "Munthu aliyense amene mwampatsa angathe kutsata ma transaction onse omwe amatumizidwa kwa iyo kwa nthawi zonse."
yourBitcoinAddressIs: "Adilesi yanu ya Bitcoin ndi:" yourBitcoinAddressIs: "Adilesi yanu ya Bitcoin ndi:"
smsOnchainAddress: "SMS onchain adilesi" smsOnchainAddress: "SMS onchain adilesi"
getNewOnchainAddress: "Pezani adilesi yatsopano ya onchain" getNewOnchainAddress: "Pezani adilesi yatsopano ya onchain"
newOnchainAddressAsFollows: "Adilesi yanu yatsopano ya Bitcoin onchain ndi monga pansipa:" newOnchainAddressAsFollows: "Adilesi yanu yatsopano ya Bitcoin onchain ili pansipa:"
youWillReceiveSMS: "Mudzalandira kudzera ku SMS ngati malire alola." youWillReceiveSMS: "Mudzalandira kudzera ku SMS ngati malire alola."
failedToGenerateOnchainAddress: "Sikunatheke kupanga adilesi yatsopano ya onchain. Chonde yesaninso." failedToGenerateOnchainAddress: "Sizinatheke kupanga adilesi yatsopano ya onchain. Chonde yeseraninso."
smsHasBeenSent: "SMS yatengedwa kwa adilesi:" smsHasBeenSent: "SMS ya adilesi yatumizidwa:"
checkInbox: "Chonde yang'anani m'bokosi lanu." checkInbox: "Chonde yang'anani m'bokosi lanu la SMS."
generateNewAddress: "Chonde pangani adilesi yatsopano. Yomwe idakali yagwiritsidwa ntchito." generateNewAddress: "Chonde pangani adilesi yatsopano. Yakaleyi yagwiritsidwa kale ntchito."
enterPin4AccountDetails: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti muwone zambiri za akaunti yanu:" enterPin4AccountDetails: "Lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti muwone zambiri za akaunti yanu:"
machankuraBalance: "Mulingo ndi {{{balance}}} {{{currencyTicker}}} (kuyerekeza kuti ili pafupi ndi {{{fiatAmount}}} {{{fiatCurrency}}})." machankuraBalance: "Ndalama zotsala ndi {{{balance}}} {{{currencyTicker}}} (pafupifupi {{{fiatAmount}}} {{{fiatCurrency}}})."
transactionHistory: "Malonda" transactionHistory: "ma transaction"
purchasedVoucher: "Wogula Voucher" purchasedVoucher: "Voucher yogulidwa"
unknown: "Sadziwika" unknown: "Zosadziwika"
transactionDetail: "Mumapereka kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} {{{counterPartyText}}} (udindo: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}" transactionDetail: "Mwatumiza kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} {{{counterPartyText}}} (womwe zilili: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
electricity: "Magetsi" electricity: "Magetsi"
electricityTransactionDetail: "Mumapereka kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} Lightning Watts (udindo: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}" electricityTransactionDetail: "Mwatumiza kapena kulandira {{{amountInSatoshis}}} {{{currencyTicker}}} {{{fromOrTo}}} Lightning Watts (momwe zilili: {{{status}}}) pa {{{dateText}}} {{{timeText}}}\n{{{redemptionInfoText}}}"
failedToProcess: "Sikunatheke kugwira ntchito malondawo." failedToProcess: "Sizinatheke."
noTransaction: "Simunachitepo ntchito ndi Machankura. Zimenezi zisintha mukatumiza kapena kulandira Bitcoin pogwiritsa ntchito Machankura." noTransaction: "Simunatumizepo kapena kulandira pa Machankura. Zimenezi zisintha mukatumiza kapena kulandira Bitcoin pogwiritsa ntchito Machankura."
select: "Sankhani:" select: "Sankhani:"
more: "zambiri" more: "zambiri"
failedTransactionHistory: "Sikunatheke kufotokozera mbiri yamalonda." failedTransactionHistory: "Sizinatheke kupereka mbiri ya akaunti."
buyUsingMachankura: "Gulani pogwiritsa ntchito Machankura" buyUsingMachankura: "Gulani pogwiritsa ntchito Machankura"
integrationComingSoon: "Kulumikizana kuti mugwiritse ntchito BTC kukubwera posachedwa." integrationComingSoon: "Kulumikizana kuti mugwiritse ntchito BTC kukubwera posachedwa."
buyAirtime: "Gulani airtime:" buyAirtime: "Gulani mayunitsi:"
forYourNumber: "Nambala yanu ({{{phoneNumber}}})" forYourNumber: "Nambala yanu ({{{phoneNumber}}})"
forAnotherNumber: "Kwa nambala ina" forAnotherNumber: "Ku nambala ina"
enterPhoneNumberForAirtime: "Lowetsani nambala ya foni yomwe mukufuna kugula airtime:" enterPhoneNumberForAirtime: "Lowetsani nambala ya foni yomwe mukufuna kugula mayunitsi:"
pickAProduct: "Sankhani chinthu" pickAProduct: "Sankhani katundu"
yourself: "inu nokha" yourself: "inu eni"
failedAirtimePinProduct: "Sikunatheke kugwira ntchito airtime pin product." failedAirtimePinProduct: "Sizinatheke kupanga pin ya mayunitsi."
enterWattsMeterNumber: "Chonde lowetsani nambala ya mita yomwe mukufuna kugula magetsi:" enterWattsMeterNumber: "Chonde lowetsani nambala ya mita yomwe mukufuna kugula magetsi:"
enterWattsAmount: "Chonde lowetsani kuchuluka kwa magetsi omwe mukufuna kugula (osachepera: 25 ZAR, osapitilira: 1 000 ZAR):" enterWattsAmount: "Chonde lowetsani kuchuluka kwa magetsi omwe mukufuna kugula (osachepera: 25 ZAR, osapitilira: 1 000 ZAR):"
enterPinForWatts: "Chonde lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{satoshis}}} sats ({{{zarAmount}}} ZAR) kwa {{{meterNumberInput}}}:" enterPinForWatts: "Chonde lowetsani PIN yanu ya Machankura kuti mugule {{{satoshis}}} sats ({{{zarAmount}}} ZAR) ku {{{meterNumberInput}}}:"
failedWattsPurchase: "Sikunatheke kupeza invoice kuti mugule magetsi kwa nambala ya mita {{{meterNumberInput}}}. Chonde yesaninso." failedWattsPurchase: "Sizinatheke kupeza invoice kuti mugule magetsi ku nambala ya mita {{{meterNumberInput}}}. Chonde yeseraninso."
initiatedWattsPurchase: "Mwayambitsa kugula {{{amountInSatoshis}}} sats ({{{amountInZAR}}} ZAR) kuti mugule magetsi kwa {{{meterNumber}}}." initiatedWattsPurchase: "Ntchito yogula {{{amountInSatoshis}}} sats ({{{amountInZAR}}} ZAR) kuti mugule magetsi ku {{{meterNumber}}}."
failedWattsPurchaseWithAmount: "Sikunatheke kuyambitsa kugula {{{amountInZAR}}} ZAR wa magetsi kwa {{{meterNumberInput}}} ku Machankura. Chonde yesaninso." failedWattsPurchaseWithAmount: "Sizinatheke kuyamba kugula {{{amountInZAR}}} ZAR wa magetsi ku {{{meterNumberInput}}} ku Machankura. Chonde yeseraninso."
wattsValidRangePrompt: "Chonde lowetsani nambala pakati pa 25 ZAR ndi 1000 ZAR." wattsValidRangePrompt: "Chonde lowetsani nambala pakati pa 25 ZAR ndi 1000 ZAR."
wattsInvalidMeterNumber: "Nambala ya mita yomwe mwalemba siyolondola. Chonde yesaninso." wattsInvalidMeterNumber: "Nambala ya mita yomwe mwalemba siyolondola. Chonde yeseraninso."
pickElectricityVendor: "Sankhani wogulitsa magetsi" pickElectricityVendor: "Sankhani wogulitsa magetsi"
pickPetrolGarage: "Sankhani gareji ya petrol" pickPetrolGarage: "Sankhani filing station/Malo omwetsera mafuta"
pickAStore: "Sankhani sitolo" pickAStore: "Sankhani sitolo"
categoryInactive: "Chigawo sichinakhalepo. Chonde yesaninso pambuyo pake." categoryInactive: "Gawo ili silinakhazikitsidwe. Chonde yeseraninso nthawi ina."
btcExchangeRate: "BTC mtengo wosinthira" btcExchangeRate: "Mtengo wosinthira BTC"
bitcoin: "Bitcoin" bitcoin: "Bitcoin"
thankYouForVisiting: "Zikomo chifukwa chobwera ku Machankura." thankYouForVisiting: "Zikomo posankha Machankura."
welcomeToMachankura: "Takulandirani ku Machankura (chikwama cha Bitcoin pa foni)" welcomeToMachankura: "Takulandirani ku Machankura (Wallet ya Bitcoin pa foni)"
welcomeToMachankuraShort: "Takulandirani ku Machankura" welcomeToMachankuraShort: "Takulandirani ku Machankura"
whatYouWantPrompt: "Mukufuna kuchita chiyani" whatYouWantPrompt: "Zomwe mukufuna kuchita"
registerAccount: "Lowetsani akaunti" registerAccount: "Tsegulani akaunti"
changeLanguage: "Sinthani Chilankhulo" changeLanguage: "Sinthani Chiyankhulo"
machankuraIsAMobileService: "Machankura ndi ntchito ya m'manja yomwe imatumiza ndikulandira Bitcoin mmalo mwanu kudzera pa nambala ya foni yanu." machankuraIsAMobileService: "Machankura ndi ntchito yapafoni ya m'manja yomwe imatumiza ndikulandira Bitcoin mmalo mwanu kudzera pa nambala ya foni yanu."
learnAboutBitcoin: "Phunzirani za Bitcoin" learnAboutBitcoin: "Phunzirani za Bitcoin"
bitcoinIsElectronicMoney: "Bitcoin ndi ndalama zamagetsi zamagulu osiyanasiyana zomwe zinayambitsidwa ndi Satoshi Nakamoto mu 2008. Ndi ndalama zokhazokha zapaintaneti." bitcoinIsElectronicMoney: "Bitcoin ndi ndalama zotumizidwa Ndi kulandiridwa ndi mphamvu yamagetsi zogwiritsidwa zoyendetsedwa Ndi kugwiritsidwa nthchito ndi wina aliyense, kwina kulikonse, nthawi iliyonse, zomwe zinayambitsidwa ndi Satoshi Nakamoto mu 2008. Ndi ndalama zokhazokha zapaintaneti."
thankYouForVisitingTillNextTime: "Zikomo chifukwa cha kuyesa Machankura. Tidzakhala okondwa kukuthandizani mukabweranso nthawi ina." thankYouForVisitingTillNextTime: "Zikomo posankha Machankura. Tidzakhala okondwa kukuthandizani mukabweranso nthawi ina."
registerAccountPrompt: "Kuti mupange akaunti ya Machankura, chonde lowetsani PIN ya 5-digit yomwe mudzagwiritse ntchito mukamagwiritsa ntchito akaunti yanu:" registerAccountPrompt: "Kuti mutsegule akaunti ya Machankura, chonde lowetsani PIN ya zilembo 5 (5-digit) yomwe kumagwiritsa ntchito ntchito akaunti yanu:"
youHaveGifts: "Muli ndi mphatso {{{giftCount}}} zomwe zikukuyembekezerani ;) (pitani ku Menyu ndikuwona zambiri za akaunti)." youHaveGifts: "Muli ndi mphatso {{{giftCount}}} zomwe zikukuyembekezerani ;) (pitani ku Menyu ndikuwona zambiri za akaunti)."
enjoySendingAndReceiving: "Sangalalani kutumiza ndi kulandira Bitcoin. ;)" enjoySendingAndReceiving: "Sangalalani kutumiza ndi kulandira Bitcoin. ;)"
accountCreated: "Tapanga akaunti yanu ya Machankura." accountCreated: "Tapanga akaunti yanu ya Machankura."
failedToCreateUser: "Sikunatheke kupanga wogwiritsa ntchito. Chonde yesaninso." failedToCreateUser: "Sizinatheke kupanga wogwiritsa ntchito. Chonde yeseraninso."
englishOnly: "Chingerezi ndiye chilankhulo chokha chomwe chilipo ku Machankura pakadali pano. Tikuwonjezera zambiri posachedwa." englishOnly: "Chingerezi ndiye chilankhulo chokha chomwe chilipo ku Machankura pakadali pano. Tikuwonjezera zambiri posachedwa."
exchangeBTC: "Sinthani BTC" exchangeBTC: "Sinthani BTC"
clans: "Mabanja" clans: "Magulu"
back: "Kubwerera" back: "Kubwerera"
enterSendMediumPrompt: "Chonde lowetsani {{{medium}}} kuti mutumize Bitcoin:" enterSendMediumPrompt: "Chonde lowetsani {{{medium}}} kuti mutumize Bitcoin:"
lightningInvoice: "LN Invoice (Bolt11)" lightningInvoice: "LN Invoice (Bolt11)"
onchain: "Onchain" onchain: "Onchain"
lightningInvoicesUnsupported: "Pepani, ma LN Invoice sathandizidwa kudzera ku USSD chifukwa nthawi zambiri amakhala otalikirapo kuti agwirizane ndi malire a zilembo 160 za USSD." lightningInvoicesUnsupported: "Pepani, ma LN Invoice palibe kudzera ku USSD chifukwa nthawi zambiri amakhala otalikirapo kuti agwirizane ndi malire a zilembo 160 za USSD."
minimumMaximumRange: "(Osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, Osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})" minimumMaximumRange: "(Osachepera: {{{minimumAmount}}} {{{currencyTicker}}}, Osapitilira: {{{maximumAmount}}} {{{currencyTicker}}})"
amountConversionText: "({{{amountInSats}}} sats = {{{amountConverted}}} {{{convertedCurrencyTicker}}})" amountConversionText: "({{{amountInSats}}} sats = {{{amountConverted}}} {{{convertedCurrencyTicker}}})"
sendBitcoinConfirmation: "Muli pafupi kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} (chindapusa cha ntchito: {{{feeText}}}{{{networkFeeText}}})." sendBitcoinConfirmation: "Muli pafupi kutumiza {{{amountText}}} kwa {{{receiver}}} (mtengo wake: {{{feeText}}}{{{networkFeeText}}})."
networkFee: "chindapusa cha netiweki: {{{networkFeeText}}} ${currencyTicker}" networkFee: "mtengo wa netiweki: {{{networkFeeText}}} ${currencyTicker}"
sendSats: "Tumizani sats" sendSats: "Tumizani ma sats"
pleaseUseWebForBolt11: "Chonde gwiritsani ntchito tsamba lawebusayiti pansipa kuti mupange (Bolt 11) Lightning Invoice ndikulandira sats ku akaunti yanu." pleaseUseWebForBolt11: "Chonde gwiritsani ntchito tsamba lawebusayiti pansipa kuti mupange (Bolt 11) Lightning Invoice ndikulandira sats ku akaunti yanu."
lightningInvoiceShort: "LN Invoice" lightningInvoiceShort: "LN Invoice"
languages: "Zilankhulo" languages: "Zilankhulo"
noOtherLanguagesAvailable: "Palibe zilankhulo zina zomwe zilipo." noOtherLanguagesAvailable: "Palibe zilankhulo zina zomwe zilipo."
changeLanguageExplanation: "Mukangosintha izi, mawu onse omwe mudzawona ku Machankura azikhala mChichewa." changeLanguageExplanation: "Mukangosintha izi, mawu onse omwe mudzawona ku Machankura azikhala mChichewa."
changeLanguagePinPrompt: "Lowetsani {{pin}} kuti musinthe chilankhulo kukhala Chichewa" changeLanguagePinPrompt: "Lowetsani {{pin}} kuti musinthe chilankhulo kukhala Chichewa"
changeLanguageConfirmation: "Sinthani chilankhulo kukhala Chichewa" changeLanguageConfirmation: "Sinthani chiyankhulo kukhala Chichewa"
cancel: "Letsani"
changeLanguageSuccessful: "Chilankhulo chogwiritsidwa ntchito ku Machankura chasinthidwa kukhala Chingerezi."
changeLanguageFailed: "Sizinatheke kusintha chilankhulo chomwe mukufuna. Chonde yeseraninso."
cancel: "Letsani" cancel: "Letsani"
changeLanguageSuccessful: "Chilankhulo chomwe chimagwiritsidwa ntchito ku Machankura chasinthidwa kukhala Chingerezi."
changeLanguageFailed: "Sikunatheke kusintha zokonda chilankhulo chomwe mukufuna. Chonde yesaninso."
account: "Akaunti" account: "Akaunti"
security: "Chitetezo" security: "Chitetezo"
noPastElectricityMeters: "Palibe manambala a mita zakale" noPastElectricityMeters: "Palibe manambala akale a mita"
thankYouForVisitingReturnToCreateAccount: "Zikomo potipatsa mwayi ku Machankura. Chonde bwererani kuti mupange akaunti." thankYouForVisitingReturnToCreateAccount: "Zikomo posankha Machankura. Chonde bwererani kuti mutsegule akaunti."
machankuraSecurityManagement: "Kusamalira Chitetezo cha Machankura:" machankuraSecurityManagement: "Kusamalira Chitetezo cha Machankura:"
accessLock: "Kutsekereza Mwayi (kufunika PIN pa ntchito)" accessLock: "Chitetezo (kufunika PIN pa ntchito)"
managePIN: "Sinthani PIN" managePIN: "Sinthani PIN"
manageAuthenticatorOTP: "Sinthani Wotsimikizira OTP" manageAuthenticatorOTP: "Sinthani ndondomeko yotsimikizira OTP"
configureAuthenticatorOTP: "Sinthani Makonzedwe a Wotsimikizira OTP" configureAuthenticatorOTP: "Ikani ndondomeko yotsimikizira OTP"
authenticatorOTP: "OTP ya Wotsimikizira" authenticatorOTP: "OTP ya Wotsimikizira"
lockAccess: "Tsekani Mwayi" lockAccess: "Tsekani Mwayi"
lockRequiredExplanation: "Kufunika kulowetsa PIN/OTP kuti mupeze sats" lockRequiredExplanation: "Kufunika kulowetsa PIN/OTP kuti mupeze sats"
lockNotRequiredExplanation: "Mungapeze sats popanda kulowetsa PIN/OTP" lockNotRequiredExplanation: "Mungapeze sats popanda kulowetsa PIN/OTP"
disableLock: "Zimitsani Kutsekereza" disableLock: "Chotsani chitetezo"
enableLock: "Yambitsani Kutsekereza" enableLock: "Ikani chitetezo"
accessLockHasBeenEnabled: "Kutsekereza kwapangidwa." accessLockHasBeenEnabled: "Chitetezo chaikidwa."
accessLockHasBeenDisabled: "Kutsekereza kwachotsedwa." accessLockHasBeenDisabled: "Chitetezo chachotsedwa."
yourMachankura: "Yanu" yourMachankura: "Yanu"
securityMechanism: "{{{your}}} {{{pinOrOTP}}}" securityMechanism: "{{{your}}} {{{pinOrOTP}}}"
accessLockHasBeenEnabledExplanation: "Tsopano muyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti mupeze sats." accessLockHasBeenEnabledExplanation: "Tsopano muyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti muone sats."
accessLockHasBeenDisabledExplanation: "Tsopano simuyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti mupeze sats." accessLockHasBeenDisabledExplanation: "Tsopano simuyenera kulowetsa {{{securityMechanism}}} kuti mupeze sats."
enterLockMechanismToSetUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti mukhazikitse dzina la wosuta pa adilesi yanu ya mphezi:" enterLockMechanismToSetUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti mukhazikitse dzina la wogwirista nthchito pa adilesi yanu ya lightning:"
enterLockMechanismToUpdateUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti musinthe dzina la wosuta la adilesi yanu ya mphezi:" enterLockMechanismToUpdateUsername: "Lowetsani {{{securityMechanism}}} kuti musinthe dzina la wosuta la adilesi yanu ya mphezi:"
accountSettings: "Zokonzekera Akaunti" accountSettings: "Zothandizira Akaunti"
deleteAccount: "Chotsani Akaunti" deleteAccount: "Chotsani Akaunti"
yourAboutToRequestAccountDelete: "Mukukonzekera kupempha kuchotsa akaunti yanu kwamuyaya:" yourAboutToRequestAccountDelete: "Mukukonzekera kupempha kuchotsa akaunti yanu kwa nthawi zonse:"
cancelledDeletingAccount: "Mwasiya njira yochotsa akaunti yanu. Zikomo potipitilira ndi Machankura." cancelledDeletingAccount: "Mwasiya nthchito yochotsa akaunti yanu. Zikomo potipitilira ndi Machankura."
deleteAccountConsequences: "Mgwirizano wonse ndi deta ya malonda ndi dongosolo yomwe ikukhudzana ndi akaunti yanu ichotsedwa:" deleteAccountConsequences: "Mgwirizano wonse ndi mbiri ya ma transaction ndi dongosolo lomwe ikukhudzana ndi akaunti yanu ichotsedwa:"
deleteAccountRequestSubmitted: "Pempho lanu lochotsa akaunti lawunikidwa. Mudzalandira zosintha zikamalizidwa." deleteAccountRequestSubmitted: "Pempho lanu lochotsa akaunti laperekedwa. Mudzalandira zosintha zikamalizidwa."
failedToSubmitDeleteAccountRequest: "Pempho lanu lochotsa akaunti lachotsedwa." failedToSubmitDeleteAccountRequest: "Pempho lanu lochotsa akaunti silinaperekedwe."
deleteAccountTODO: "Ntchito yochotsa akaunti siyinathe." deleteAccountTODO: "Ntchito yochotsa akaunti siyinathe."
functionalityComingSoon: "Ntchito ikubwera posachedwa." functionalityComingSoon: "Ntchito ikubwera posachedwa."
createAccountExplanation: "Mukakhazikitsa akaunti ya Machankura, mutha kutumiza ndi kulandira Bitcoin:" createAccountExplanation: "Mukakhazikitsa akaunti ya Machankura, mutha kutumiza ndi kulandira Bitcoin:"